Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 11:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Yehova Mulungu wanu akadzakulowetsani mʼdziko limene mukupita kukalitenga kuti likhale lanu, mukatchule dalitsoli paphiri la Gerizimu ndipo temberero mukalitchulire* paphiri la Ebala.+

  • Yoswa 8:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Aisiraeli onse, atsogoleri awo, akapitawo awo, ndi oweruza awo anasonkhanitsidwa pamodzi. Panalinso alendo ndi nzika.+ Ena anaima mbali iyi ya Likasa, ena anaima mbali inayo, pamaso pa Alevi omwe anali ansembe amene ananyamula likasa la pangano la Yehova. Hafu ya anthuwo inaima mʼphiri la Gerizimu, ndipo hafu ina inaima mʼphiri la Ebala,+ (ngati mmene Mose mtumiki wa Yehova analamulira),+ kuti Aisiraeliwo adalitsidwe.

  • Yohane 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Makolo athu ankalambira mʼphiri ili, koma anthu inu mumanena kuti malo amene anthu akuyenera kulambirirako Mulungu ali ku Yerusalemu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena