Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 18:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anthu a fuko la Dani anatumiza amuna 5 a mʼbanja lawo, amuna olimba mtima ochokera ku Zora ndi ku Esitaoli+ kuti akafufuze zokhudza malowo. Anawauza kuti: “Pitani mukafufuze zokhudza malowo.” Atafika kudera lamapiri la Efuraimu, kunyumba ya Mika,+ anagona kumeneko.

  • Oweruza 18:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Kuwonjezera apo, mzindawu anaupatsa dzina loti Dani,+ kutengera dzina la bambo awo lakuti Dani, amene anali mwana wa Isiraeli.+ Koma dzina loyamba la mzindawu linali Laisi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena