Oweruza 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuwonjezera pamenepo, Mika anapatsa Mleviyo udindo woti akhale wansembe wake+ ndipo ankakhala mʼnyumba ya Mikayo.
12 Kuwonjezera pamenepo, Mika anapatsa Mleviyo udindo woti akhale wansembe wake+ ndipo ankakhala mʼnyumba ya Mikayo.