Yoswa 5:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Atamaliza kudula amuna onse, aliyense anakhalabe muhema wake pamsasapo mpaka atachira. 9 Kenako Yehova anauza Yoswa kuti: “Lero ndachititsa kuti Aiguputo asamakunyozeninso.”* Choncho malowo amawatchula kuti Giligala,*+ mpaka lero.
8 Atamaliza kudula amuna onse, aliyense anakhalabe muhema wake pamsasapo mpaka atachira. 9 Kenako Yehova anauza Yoswa kuti: “Lero ndachititsa kuti Aiguputo asamakunyozeninso.”* Choncho malowo amawatchula kuti Giligala,*+ mpaka lero.