Oweruza 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma ife sitikuloledwa kuwapatsa ana athu aakazi kuti akhale akazi awo, chifukwa Aisiraeli analumbira kuti, ‘Aliyense wopereka mkazi kwa mwamuna wa fuko la Benjamini ndi wotembereredwa.’”+
18 Koma ife sitikuloledwa kuwapatsa ana athu aakazi kuti akhale akazi awo, chifukwa Aisiraeli analumbira kuti, ‘Aliyense wopereka mkazi kwa mwamuna wa fuko la Benjamini ndi wotembereredwa.’”+