Oweruza 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo Aisiraeli anapita ku Beteli kukafunsa kwa Mulungu+ kuti: “Ndani akuyenera kutitsogolera kunkhondo yokamenyana ndi fuko la Benjamini?” Yehova anayankha kuti: “Yuda akutsogolereni.” Oweruza 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zitatero, amuna onse a Isiraeli anapita ku Beteli. Kumeneko analira nʼkukhala pansi pamaso pa Yehova+ ndipo anasala kudya+ mpaka madzulo. Iwo anapereka kwa Yehova nsembe zopsereza+ ndi nsembe zamgwirizano.+
18 Ndipo Aisiraeli anapita ku Beteli kukafunsa kwa Mulungu+ kuti: “Ndani akuyenera kutitsogolera kunkhondo yokamenyana ndi fuko la Benjamini?” Yehova anayankha kuti: “Yuda akutsogolereni.”
26 Zitatero, amuna onse a Isiraeli anapita ku Beteli. Kumeneko analira nʼkukhala pansi pamaso pa Yehova+ ndipo anasala kudya+ mpaka madzulo. Iwo anapereka kwa Yehova nsembe zopsereza+ ndi nsembe zamgwirizano.+