Yoswa 24:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Atatero, Yoswa anauza anthuwo kuti azipita, aliyense kucholowa chake.+