Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Choncho Aisiraeli anayamba kuchita zoipa pamaso pa Yehova ndipo anaiwala Yehova Mulungu wawo. Iwo ankalambiranso Abaala+ ndi mizati yopatulika.*+

  • Oweruza 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Aisiraeli anayambanso kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ ndipo anayamba kutumikira Abaala,+ mafano a Asitoreti, milungu ya ku Aramu,* milungu ya ku Sidoni, milungu ya ku Mowabu,+ milungu ya Aamoni+ ndi milungu ya Afilisiti.+ Iwo anasiya Yehova ndipo sankamutumikira.

  • 1 Mafumu 18:17, 18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ahabu atangoona Eliya, anati: “Kodi ndiwe eti? Iwe ndi amene wabweretsa mavuto ambiri mu Isiraeli.”

      18 Eliya anayankha kuti: “Ine sindinabweretse mavuto mu Isiraeli, koma inuyo ndi nyumba ya bambo anu. Chifukwa mwasiya kutsatira malamulo a Yehova nʼkuyamba kutsatira Abaala.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena