Oweruza 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aisiraeli atafuulira Yehova kuti awathandize,+ Yehova anawapatsa munthu woti awapulumutse.+ Munthu wake anali Otiniyeli,+ mwana wamwamuna wa Kenazi, mngʼono wake wa Kalebe. 1 Samueli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Yehova anatumiza Yerubaala,+ Bedani, Yefita+ ndi Samueli+ ndipo anakupulumutsani kwa adani anu onse okuzungulirani kuti mukhale pa mtendere.+ Nehemiya 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chifukwa cha zimenezi, munawapereka mʼmanja mwa adani awo+ amene ankawazunza.+ Koma akakumana ndi mavuto ankakulirirani ndipo inu munkamva muli kumwambako. Chifukwa cha chifundo chanu chachikulu, munkawapatsa anthu oti awapulumutse mʼmanja mwa adani awo.+ Salimo 106:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Nthawi zambiri ankawapulumutsa,+Koma iwo ankamupandukira komanso sankamvera,+Ndipo ankawonongedwa chifukwa cha zolakwa zawo.+
9 Aisiraeli atafuulira Yehova kuti awathandize,+ Yehova anawapatsa munthu woti awapulumutse.+ Munthu wake anali Otiniyeli,+ mwana wamwamuna wa Kenazi, mngʼono wake wa Kalebe.
11 Kenako Yehova anatumiza Yerubaala,+ Bedani, Yefita+ ndi Samueli+ ndipo anakupulumutsani kwa adani anu onse okuzungulirani kuti mukhale pa mtendere.+
27 Chifukwa cha zimenezi, munawapereka mʼmanja mwa adani awo+ amene ankawazunza.+ Koma akakumana ndi mavuto ankakulirirani ndipo inu munkamva muli kumwambako. Chifukwa cha chifundo chanu chachikulu, munkawapatsa anthu oti awapulumutse mʼmanja mwa adani awo.+
43 Nthawi zambiri ankawapulumutsa,+Koma iwo ankamupandukira komanso sankamvera,+Ndipo ankawonongedwa chifukwa cha zolakwa zawo.+