Oweruza 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aisiraeli atafuulira Yehova kuti awathandize,+ Yehova anawapatsa munthu woti awapulumutse.+ Munthu wake anali Otiniyeli,+ mwana wamwamuna wa Kenazi, mngʼono wake wa Kalebe.
9 Aisiraeli atafuulira Yehova kuti awathandize,+ Yehova anawapatsa munthu woti awapulumutse.+ Munthu wake anali Otiniyeli,+ mwana wamwamuna wa Kenazi, mngʼono wake wa Kalebe.