Deuteronomo 32:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pakuti Yehova adzaweruza anthu ake,+Ndipo adzamvera chisoni atumiki ake+Akadzaona kuti mphamvu zawo zatha,Komanso kuti kwangotsala anthu ovutika ndi ofooka. Salimo 106:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Pofuna kuwathandiza iye ankakumbukira pangano lake,Ndipo ankawamvera chisoni* chifukwa cha chikondi chake chokhulupirika chomwe ndi chachikulu.*+
36 Pakuti Yehova adzaweruza anthu ake,+Ndipo adzamvera chisoni atumiki ake+Akadzaona kuti mphamvu zawo zatha,Komanso kuti kwangotsala anthu ovutika ndi ofooka.
45 Pofuna kuwathandiza iye ankakumbukira pangano lake,Ndipo ankawamvera chisoni* chifukwa cha chikondi chake chokhulupirika chomwe ndi chachikulu.*+