-
Rute 1:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Patapita nthawi, Elimeleki mwamuna wa Naomi anamwalira ndipo Naomi anatsala ndi ana ake aja.
-
-
Rute 1:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Patapita nthawi, ana awiriwo, Maloni ndi Kiliyoni, nawonso anamwalira, ndipo Naomi anatsala yekha wopanda ana komanso mwamuna.
-