Rute 1:3, 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Patapita nthawi, Elimeleki mwamuna wa Naomi anamwalira ndipo Naomi anatsala ndi ana ake aja. 4 Kenako anawo anakwatira akazi a Chimowabu. Wina dzina lake anali Olipa ndipo wina anali Rute.+ Iwo anakhalabe kumeneko zaka pafupifupi 10.
3 Patapita nthawi, Elimeleki mwamuna wa Naomi anamwalira ndipo Naomi anatsala ndi ana ake aja. 4 Kenako anawo anakwatira akazi a Chimowabu. Wina dzina lake anali Olipa ndipo wina anali Rute.+ Iwo anakhalabe kumeneko zaka pafupifupi 10.