16 Koma Rute anati: “Musandichonderere kuti ndikusiyeni, kuti ndibwerere ndisakutsatireni, chifukwa kumene inu mupite inenso ndipita komweko ndipo kumene mugone inenso ndigona komweko. Anthu a mtundu wanu adzakhala anthu a mtundu wanga ndipo Mulungu wanu adzakhala Mulungu wanga.+