Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 19:36, 37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Choncho ana a Loti awiri onsewo anakhala oyembekezera atagona ndi bambo awo. 37 Mwana woyamba anabereka mwana wamwamuna nʼkumupatsa dzina lakuti Mowabu.+ Iye ndi tate wa Amowabu amasiku ano.+

  • Deuteronomo 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno Yehova anandiuza kuti, ‘Usalimbane ndi Amowabu kapena kuchita nawo nkhondo, chifukwa sindidzakupatsa mbali iliyonse ya dziko lawo kuti likhale lako. Ndinapereka Ari kwa mbadwa za Loti+ kuti akhale malo awo.

  • Oweruza 3:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Choncho pa tsiku limenelo, Aisiraeli anagonjetsa Amowabu, ndipo dzikolo linakhala pa mtendere zaka 80.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena