Rute 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atafika anapempha kuti, ‘Ndimati ndikunkhe nawo.+ Ndizitola balere* wotsala pambuyo pa anthu amene akukololawa.’ Ndipo wakhala akukunkha kuyambira mʼmawa mpaka posachedwapa pamene anakhala pamthunzi kuti apume pangʼono.”
7 Atafika anapempha kuti, ‘Ndimati ndikunkhe nawo.+ Ndizitola balere* wotsala pambuyo pa anthu amene akukololawa.’ Ndipo wakhala akukunkha kuyambira mʼmawa mpaka posachedwapa pamene anakhala pamthunzi kuti apume pangʼono.”