Rute 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Izi ndi zomwe zinachitika pamene Naomi ankabwerera kwawo kuchokera ku Mowabu.+ Iye anabwerera ndi mpongozi wake Rute wa ku Mowabu. Iwo anafika ku Betelehemu kumayambiriro kwa nthawi yokolola balere.+
22 Izi ndi zomwe zinachitika pamene Naomi ankabwerera kwawo kuchokera ku Mowabu.+ Iye anabwerera ndi mpongozi wake Rute wa ku Mowabu. Iwo anafika ku Betelehemu kumayambiriro kwa nthawi yokolola balere.+