Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ine ndidzadutsa mʼdziko la Iguputo usiku umenewo nʼkupha mwana aliyense woyamba kubadwa mʼdziko la Iguputo, mwana wa munthu kapena wa chiweto.+ Ndipo ndidzapereka chiweruzo pa milungu yonse ya mu Iguputo.+ Ine ndine Yehova.

  • 1 Mbiri 16:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake.+

      Koma Yehova ndi amene anapanga kumwamba.+

  • Salimo 97:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Onse amene akutumikira chifaniziro chilichonse achite manyazi,+

      Amene amadzitama chifukwa cha milungu yawo yopanda pake.+

      Muweramireni,* inu milungu yonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena