-
1 Samueli 6:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mupange zifaniziro za matenda anu a mudzi ndi zifaniziro za mbewa+ zimene zikuwononga dziko, ndipo muyenera kulemekeza Mulungu wa Isiraeli. Mukatero, mwina adzachepetsako mphamvu ya dzanja lake kwa inuyo, mulungu wanu ndi dziko lanu.+ 6 Nʼchifukwa chiyani mukuumitsa mitima yanu ngati mmene anachitira Aiguputo ndi Farao?+ Mulungu atawakhaulitsa+ analola Aisiraeli kupita ndipo iwo anapitadi.+
-