1 Samueli 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno kumsasa wa Afilisiti kunatuluka ngwazi,* dzina lake Goliyati,+ wa ku Gati.+ Iye anali wamtali pafupifupi mamita atatu.*
4 Ndiyeno kumsasa wa Afilisiti kunatuluka ngwazi,* dzina lake Goliyati,+ wa ku Gati.+ Iye anali wamtali pafupifupi mamita atatu.*