1 Mbiri 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho anabweretsa Likasa la Mulungu woona pamalo amene Davide anakonza nʼkuliika mutenti imene iye anamanga kuti lizikhalamo.+ Kenako iwo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano kwa Mulungu woona.+ 2 Mbiri 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Davide anali atachotsa Likasa la Mulungu woona ku Kiriyati-yearimu+ nʼkukaliika pamalo amene anakonza. Iye anali atamanga tenti ya Likasalo ku Yerusalemu.+
16 Choncho anabweretsa Likasa la Mulungu woona pamalo amene Davide anakonza nʼkuliika mutenti imene iye anamanga kuti lizikhalamo.+ Kenako iwo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano kwa Mulungu woona.+
4 Koma Davide anali atachotsa Likasa la Mulungu woona ku Kiriyati-yearimu+ nʼkukaliika pamalo amene anakonza. Iye anali atamanga tenti ya Likasalo ku Yerusalemu.+