16 “Mawa cha nthawi ngati ino ndidzakutumizira munthu kuchokera kudera la Benjamini.+ Udzamudzoze kuti akhale mtsogoleri wa anthu anga Aisiraeli.+ Iye adzapulumutsa anthu anga mʼmanja mwa Afilisiti, chifukwa ndaona mmene akuvutikira ndiponso ndamva kulira kwawo.”+