1 Samueli 7:15, 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Samueli anapitiriza kuweruza Isiraeli kwa moyo wake wonse.+ 16 Chaka chilichonse Samueli ankapita ku Beteli,+ Giligala+ ndi Mizipa+ ndipo ankaweruza Aisiraeli mʼmadera onsewa. 1 Samueli 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Samueli anauza anthuwo kuti: “Tiyeni tipite ku Giligala+ kuti tikachitenso mwambo wolonga mfumu.”+
15 Samueli anapitiriza kuweruza Isiraeli kwa moyo wake wonse.+ 16 Chaka chilichonse Samueli ankapita ku Beteli,+ Giligala+ ndi Mizipa+ ndipo ankaweruza Aisiraeli mʼmadera onsewa.
14 Kenako Samueli anauza anthuwo kuti: “Tiyeni tipite ku Giligala+ kuti tikachitenso mwambo wolonga mfumu.”+