Salimo 91:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa adzalamula angelo ake+ zokhudza iwe,Kuti akuteteze mʼnjira zako zonse.+ Salimo 97:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu amene mumakonda Yehova, muzidana ndi zoipa.+ Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawapulumutsa mʼmanja mwa* oipa.+ Salimo 121:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye sadzalola kuti phazi lako literereke.*+ Amene akukuyangʼanira sadzawodzera.
10 Inu amene mumakonda Yehova, muzidana ndi zoipa.+ Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawapulumutsa mʼmanja mwa* oipa.+