17 Isimaeli anakhala ndi moyo zaka 137. Kenako anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ake. 18 Mbadwa zake zinayamba kukhala ku Havila+ pafupi ndi Shura+ moyandikana ndi Iguputo, mpaka ku Asuri. Iwo anakhala pafupi ndi abale awo onse.+