18 Abisalomu ali moyo, anamanga chipilala chake mʼChigwa cha Mfumu,+ popeza iye anati: “Ine ndilibe mwana wamwamuna woti asunge dzina langa kuti ndizikumbukiridwa.”+ Choncho chipilalacho anachipatsa dzina lake ndipo chikudziwikabe ndi dzina lakuti Chipilala cha Abisalomu mpaka lero.