Deuteronomo 25:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiye Yehova Mulungu wanu akadzakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala cholowa chanu,+ mudzafafanize dzina la Aamaleki pansi pa thambo.+ Musadzaiwale zimenezi.
19 Ndiye Yehova Mulungu wanu akadzakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala cholowa chanu,+ mudzafafanize dzina la Aamaleki pansi pa thambo.+ Musadzaiwale zimenezi.