1 Samueli 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atatero Sauli anati: “Ndachimwa. Komabe, chonde ndilemekezeni pamaso pa akulu a anthu anga ndi Aisiraeli. Tiyeni tibwerere limodzi ndikalambire Yehova Mulungu wanu.”+
30 Atatero Sauli anati: “Ndachimwa. Komabe, chonde ndilemekezeni pamaso pa akulu a anthu anga ndi Aisiraeli. Tiyeni tibwerere limodzi ndikalambire Yehova Mulungu wanu.”+