Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma tsopano ufumu wako sukhalitsa.+ Yehova apeza munthu wapamtima pake,+ ndipo Yehova amuika kukhala mtsogoleri wa anthu ake+ chifukwa iwe sunamvere zimene Yehova anakulamula.”+

  • 1 Samueli 16:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Patapita nthawi, Yehova anauza Samueli kuti: “Kodi ulirira Sauli mpaka liti,+ munthu woti ine ndamukana kuti akhale mfumu ya Isiraeli?+ Thira mafuta mʼnyanga* yako+ ndipo unyamuke. Ndikutumiza kwa Jese+ wa ku Betelehemu, chifukwa ndasankha mmodzi wa ana ake aamuna kuti akhale mfumu yanga.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena