-
Levitiko 7:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Aliyense amene wadya mafuta a nyama imene waipereka kwa Yehova ngati nsembe yowotcha pamoto, aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu a mtundu wake.
-