1 Samueli 1:27, 28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndinkapempha kuti andipatse mwana wamwamunayu ndipo Yehova wandipatsa zimene ndinapempha.+ 28 Ndipo ine ndikumupereka kwa Yehova. Ndikumupereka kwa Yehova masiku onse a moyo wake.” Kenako iye* anagwada nʼkulambira Yehova.
27 Ndinkapempha kuti andipatse mwana wamwamunayu ndipo Yehova wandipatsa zimene ndinapempha.+ 28 Ndipo ine ndikumupereka kwa Yehova. Ndikumupereka kwa Yehova masiku onse a moyo wake.” Kenako iye* anagwada nʼkulambira Yehova.