Ekisodo 28:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Aroni ndi ana ake azivala makabudula amenewa polowa mʼchihema chokumanako kapena popita kuguwa lansembe kukatumikira pamalo oyera kuti asapalamule mlandu nʼkufa. Limeneli ndi lamulo kwa iye ndi mbadwa* zake mpaka kalekale.”
43 Aroni ndi ana ake azivala makabudula amenewa polowa mʼchihema chokumanako kapena popita kuguwa lansembe kukatumikira pamalo oyera kuti asapalamule mlandu nʼkufa. Limeneli ndi lamulo kwa iye ndi mbadwa* zake mpaka kalekale.”