-
1 Samueli 4:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Munthuyo atangotchula za Likasa la Mulungu woona, Eli, yemwe anali pageti anagwa chagada kuchoka pampando. Khosi lake linathyoka ndipo anafa chifukwa anali wokalamba ndiponso wonenepa kwambiri. Eli anaweruza Isiraeli kwa zaka 40.
-