1 Samueli 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zimenezi zinangochititsanso kuti Sauli azimuopa kwambiri Davide ndipo Sauli anakhala mdani wa Davide moyo wake wonse.+ 1 Samueli 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mukafufuze nʼkudziwa malo onse obisika kumene iye akubisala, ndipo mukabwere ndi umboni. Kenako ndidzapita nanu ndipo ngati alidi kumeneko, ndidzamʼfufuza pakati pa anthu masauzande* a ku Yuda.”
29 Zimenezi zinangochititsanso kuti Sauli azimuopa kwambiri Davide ndipo Sauli anakhala mdani wa Davide moyo wake wonse.+
23 Mukafufuze nʼkudziwa malo onse obisika kumene iye akubisala, ndipo mukabwere ndi umboni. Kenako ndidzapita nanu ndipo ngati alidi kumeneko, ndidzamʼfufuza pakati pa anthu masauzande* a ku Yuda.”