12 Timina anali mkazi wamngʼono wa Elifazi mwana wa Esau. Patapita nthawi, Timina anaberekera Elifazi mwana wamwamuna dzina lake Amaleki.+ Ana a Ada mkazi wa Esau anali amenewa.
29 Aamaleki+ akukhala ku Negebu.+ Ahiti, Ayebusi+ ndi Aamori+ akukhala kudera lamapiri. Akanani+ akukhala mʼmphepete mwa nyanja+ ndi mʼmphepete mwa mtsinje wa Yorodano.”