2 Samueli 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Mefiboseti ankakhala ku Yerusalemu ndipo ankadya patebulo la mfumu nthawi zonse.+ Iye anali wolumala mapazi.+ 1 Mbiri 8:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mwana wa Yonatani anali Meribi-baala*+ ndipo Meribi-baala anabereka Mika.+
13 Choncho Mefiboseti ankakhala ku Yerusalemu ndipo ankadya patebulo la mfumu nthawi zonse.+ Iye anali wolumala mapazi.+