1 Samueli 18:28, 29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Sauli anazindikira kuti Yehova ali ndi Davide.+ Anazindikiranso kuti mwana wake Mikala, ankamukonda kwambiri Davideyo.+ 29 Zimenezi zinangochititsanso kuti Sauli azimuopa kwambiri Davide ndipo Sauli anakhala mdani wa Davide moyo wake wonse.+
28 Sauli anazindikira kuti Yehova ali ndi Davide.+ Anazindikiranso kuti mwana wake Mikala, ankamukonda kwambiri Davideyo.+ 29 Zimenezi zinangochititsanso kuti Sauli azimuopa kwambiri Davide ndipo Sauli anakhala mdani wa Davide moyo wake wonse.+