-
1 Samueli 18:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Tsiku lotsatira, Sauli anagwidwa ndi mzimu woipa wochokera kwa Mulungu+ moti anayamba kuchita zinthu zachilendo* mʼnyumba mwake. Pa nthawiyi nʼkuti Davide akuimba nyimbo ndi zeze+ ngati mmene ankachitira ndipo Sauli anali ndi mkondo mʼmanja mwake.+ 11 Kenako Sauli anaponya mkondowo+ ndipo mumtima mwake ankati: ‘Ndibaya Davide nʼkumukhomerera kukhoma!’ Koma Davide anazinda nʼkuthawa ndipo zimenezi zinachitika kawiri konse.
-