Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 24:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Yehova aweruze pakati pa ine ndi inu,+ ndipo Yehova abwezere mʼmalo mwa ine,+ koma dzanja langali silidzakuchitirani choipa.+

  • 1 Samueli 26:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndiyeno Sauli anayankha Davide kuti: “Mulungu akudalitse mwana wanga Davide. Mosakayikira iwe udzachita ntchito zazikulu komanso zidzakuyendera bwino.”+ Zitatero, Davide anachoka ndipo Sauli anabwerera kwawo.+

  • 2 Samueli 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno Natani anauza Davide kuti: “Munthu ameneyu ndi iweyo. Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndinakudzoza kuti ukhale mfumu ya Isiraeli+ ndipo ndinakupulumutsa mʼmanja mwa Sauli.+

  • Salimo 34:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Mngelo wa Yehova amamanga msasa kuzungulira anthu onse amene amaopa Mulungu,+

      Ndipo amawapulumutsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena