-
2 Samueli 1:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Tsiku lachitatu, munthu wina anabwera kuchokera kumsasa wa Sauli. Iye anali atangʼamba zovala zake komanso atadzithira dothi kumutu. Atafika kwa Davide, anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake kufika pansi, kenako anagona pansi.
-