Deuteronomo 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma iye asakhale ndi mahatchi ambiri+ kapena kuchititsa anthu kuti abwerere ku Iguputo kuti akatenge mahatchi ochuluka+ chifukwa Yehova anakuuzani kuti, ‘Musabwererenso kudzera njira iyi.’ Salimo 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ena amadalira magaleta ndipo ena amadalira mahatchi,+Koma ife timadalira dzina la Yehova Mulungu wathu.+ Salimo 33:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Si nzeru kudalira hatchi chifukwa singapulumutse munthu,+Mphamvu zake zochuluka sizingapulumutse munthu
16 Koma iye asakhale ndi mahatchi ambiri+ kapena kuchititsa anthu kuti abwerere ku Iguputo kuti akatenge mahatchi ochuluka+ chifukwa Yehova anakuuzani kuti, ‘Musabwererenso kudzera njira iyi.’
7 Ena amadalira magaleta ndipo ena amadalira mahatchi,+Koma ife timadalira dzina la Yehova Mulungu wathu.+
17 Si nzeru kudalira hatchi chifukwa singapulumutse munthu,+Mphamvu zake zochuluka sizingapulumutse munthu