-
1 Mbiri 18:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Asiriya a ku Damasiko atabwera kudzathandiza Hadadezeri mfumu ya Zoba, Davide anapha Asiriya 22,000.+ 6 Kenako Davide anamanga midzi ya asilikali mʼdera la Asiriya a ku Damasiko ndipo Asiriyawo anakhala akapolo a Davide moti ankapereka msonkho kwa iye. Yehova ankathandiza Davide kuti apambane kulikonse kumene wapita.+
-