Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 25:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Yehova anamuyankha kuti: “Mʼmimba mwako muli mitundu iwiri ya anthu+ ndipo mitundu iwiri imene idzatuluke mʼmimba mwako idzapita kosiyana.+ Mtundu wina udzakhala wamphamvu kuposa mtundu winawo,+ ndipo wamkulu adzatumikira wamngʼono.”+

  • Genesis 25:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pambuyo pake, mʼbale wake anabadwa, ndipo dzanja lake linali litagwira chidendene cha Esau.+ Choncho Isaki anapatsa mwanayo dzina lakuti Yakobo.*+ Pamene Rabeka ankabereka anawa nʼkuti Isaki ali ndi zaka 60.

  • Genesis 27:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Mafuko akutumikire ndipo mitundu ya anthu ikugwadire. Ukhale mbuye wa abale ako, ndipo ana a mayi ako akugwadire.+ Aliyense wokutemberera atembereredwe, ndipo aliyense wokudalitsa adalitsidwe.”+

  • Genesis 27:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Koma Isaki anayankha Esau kuti: “Taona, iye uja ndamuika kukhala mbuye wako.+ Ndamupatsa abale ake onse kuti akhale atumiki ake. Komanso ndamudalitsa kuti akhale ndi zokolola zambiri ndiponso vinyo watsopano wambiri.+ Nanga chatsalanso nʼchiyani choti ndikuchitire mwana wanga?”

  • Numeri 24:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Edomu adzalandidwa,+

      Ndithu Seiri+ adzalandidwa ndi adani ake,+

      Pamene Isiraeli akuonetsa kulimba mtima kwake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena