2 Samueli 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Adoramu+ ankatsogolera anthu olembedwa ntchito yokakamiza ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi ankalemba zimene zachitika. 1 Mafumu 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Elihorefi ndi Ahiya ana a Sisa anali alembi,+ ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika.
24 Adoramu+ ankatsogolera anthu olembedwa ntchito yokakamiza ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi ankalemba zimene zachitika.
3 Elihorefi ndi Ahiya ana a Sisa anali alembi,+ ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika.