Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 19:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Choncho ana a Loti awiri onsewo anakhala oyembekezera atagona ndi bambo awo.

  • Genesis 19:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Mwana wamngʼono nayenso anabereka mwana wamwamuna nʼkumupatsa dzina lakuti Beni-ami. Iye ndi tate wa Aamoni+ amasiku ano.

  • Oweruza 10:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Zitatero, Yehova anakwiyira kwambiri Aisiraeli moti anawapereka* kwa Afilisiti ndi kwa Aamoni.+

  • Oweruza 11:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kenako Yefita anatumiza uthenga kwa mfumu ya Aamoni+ wakuti: “Ndakuyambani chiyani kuti mubwere kwathu kuno kudzamenyana nane?”

  • Oweruza 11:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Iye anapha Aamoni ambirimbiri mʼmizinda 20, kuyambira ku Aroweli mpaka ku Miniti ndipo anakafikanso ku Abele-kerami. Choncho Aisiraeli anagonjetsa Aamoni.

  • 1 Samueli 11:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno Nahasi Muamoni+ anapita kukamanga msasa kuti amenyane ndi mzinda wa Yabesi+ ku Giliyadi. Zitatero, amuna onse a ku Yabesi anauza Nahasi kuti: “Tiyeni tichite pangano* ndipo tizikutumikirani.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena