Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 26:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno Davide anauza Ahimeleki Muhiti+ ndi Abisai+ mwana wa Zeruya,+ mchimwene wake wa Yowabu, kuti: “Ndani apite nane kwa Sauli kumsasa?” Abisai anayankha kuti: “Ine ndipita nanu.”

  • 2 Samueli 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ana atatu aamuna a Zeruya,+ omwe ndi Yowabu,+ Abisai+ ndi Asaheli+ analinso pompo. Asaheli anali waliwiro kwambiri ngati mbawala.

  • 2 Samueli 23:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Abisai,+ mchimwene wake wa Yowabu mwana wa Zeruya+ anali mtsogoleri wa anthu ena atatu. Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 300. Abisai anali wotchuka ngati amuna atatu aja.+

  • 1 Mbiri 2:15, 16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 wa 6 Ozemu ndipo wa 7 anali Davide.+ 16 Azichemwali awo anali Zeruya ndi Abigayeli.+ Zeruya anali ndi ana atatu: Abisai,+ Yowabu+ ndi Asaheli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena