Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 20:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Mukapita kunkhondo kukamenyana ndi adani anu, nʼkuona kuti ali ndi mahatchi, magaleta ankhondo komanso asilikali ochuluka kuposa inu, musachite nawo mantha chifukwa Yehova Mulungu wanu, amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo ali ndi inu.+

  • Salimo 18:37, 38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Ndidzathamangitsa adani anga nʼkuwapeza,

      Sindidzabwerera mpaka onse nditawawononga.

      38 Ndidzawaphwanya kuti asadzukenso.+

      Ndidzawapondaponda ndi mapazi anga.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena