2 Samueli 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Benaya+ mwana wa Yehoyada anali mtsogoleri wa Akereti ndi Apeleti.+ Ana aamuna a Davide anali nduna zazikulu za mfumu.* 2 Samueli 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno atumiki onse a mfumu amene ananyamuka nawo limodzi, Akereti onse, Apeleti+ onse, Agiti+ onse ndiponso amuna 600 amene anamutsatira* kuchokera ku Gati+ anayamba kudutsa kutsogolo kwa mfumuyo kuti idziwe anthu amene alipo. 1 Mafumu 1:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako wansembe Zadoki, mneneri Natani, Benaya+ mwana wa Yehoyada, Akereti ndi Apeleti+ anapita kukakweza Solomo panyulu ya Mfumu Davide+ nʼkupita naye ku Gihoni.+
18 Benaya+ mwana wa Yehoyada anali mtsogoleri wa Akereti ndi Apeleti.+ Ana aamuna a Davide anali nduna zazikulu za mfumu.*
18 Ndiyeno atumiki onse a mfumu amene ananyamuka nawo limodzi, Akereti onse, Apeleti+ onse, Agiti+ onse ndiponso amuna 600 amene anamutsatira* kuchokera ku Gati+ anayamba kudutsa kutsogolo kwa mfumuyo kuti idziwe anthu amene alipo.
38 Kenako wansembe Zadoki, mneneri Natani, Benaya+ mwana wa Yehoyada, Akereti ndi Apeleti+ anapita kukakweza Solomo panyulu ya Mfumu Davide+ nʼkupita naye ku Gihoni.+