1 Mafumu 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Beni-hadadi anamvera Mfumu Asa ndipo anatumiza akuluakulu a asilikali ake kuti akamenyane ndi anthu amʼmizinda ya Isiraeli. Iwo analanda Iyoni,+ Dani,+ Abele-beti-maaka ndi Kinereti yense komanso dera lonse la Nafitali. 2 Mafumu 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mʼmasiku a Peka mfumu ya Isiraeli, Tigilati-pilesere+ mfumu ya Asuri anabwera nʼkulanda Iyoni, Abele-beti-maaka,+ Yanoa, Kedesi,+ Hazori, Giliyadi+ ndi Galileya, dera lonse la Nafitali.+ Anatenga anthu akumeneku nʼkupita nawo ku Asuri.+
20 Beni-hadadi anamvera Mfumu Asa ndipo anatumiza akuluakulu a asilikali ake kuti akamenyane ndi anthu amʼmizinda ya Isiraeli. Iwo analanda Iyoni,+ Dani,+ Abele-beti-maaka ndi Kinereti yense komanso dera lonse la Nafitali.
29 Mʼmasiku a Peka mfumu ya Isiraeli, Tigilati-pilesere+ mfumu ya Asuri anabwera nʼkulanda Iyoni, Abele-beti-maaka,+ Yanoa, Kedesi,+ Hazori, Giliyadi+ ndi Galileya, dera lonse la Nafitali.+ Anatenga anthu akumeneku nʼkupita nawo ku Asuri.+