2 Samueli 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Husai anauza Zadoki ndi Abiyatara+ ansembe kuti: “Ahitofeli wapereka malangizo akutiakuti kwa Abisalomu ndi akulu a Isiraeli koma ine ndapereka malangizo akutiakuti. 2 Samueli 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumu Davide inatumiza uthenga kwa Zadoki+ ndi Abiyatara+ ansembe wakuti: “Muwafunse akulu a Yuda+ kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani inu nokha simukuchita chilichonse kuti mfumu ibwerere kunyumba yake, pamene Aisiraeli onse atumiza uthenga kwa mfumu? 1 Mafumu 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Benaya+ mwana wa Yehoyada anali mkulu wa asilikali, ndipo Zadoki ndi Abiyatara+ anali ansembe.
15 Kenako Husai anauza Zadoki ndi Abiyatara+ ansembe kuti: “Ahitofeli wapereka malangizo akutiakuti kwa Abisalomu ndi akulu a Isiraeli koma ine ndapereka malangizo akutiakuti.
11 Mfumu Davide inatumiza uthenga kwa Zadoki+ ndi Abiyatara+ ansembe wakuti: “Muwafunse akulu a Yuda+ kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani inu nokha simukuchita chilichonse kuti mfumu ibwerere kunyumba yake, pamene Aisiraeli onse atumiza uthenga kwa mfumu?